Welcome/ Takulandirani/ Welkom Print

Steven Paas with dictionaryMy name is Steven Paas (MTh, PhD -Theology), church historian and researcher of Chichewa/ Chinyanja. On behalf of Foundation Heart for Malawi I welcome you to this site, which offers information on our Chichewa/ Chinyanja Dictionary Project. The Third Edition of the Dictionary, into and from English (884 pages, February 2012), is a hard cover large-page high quality book, and it is universally available. The Fourth Edition (1152 pages, August 2013), especially for Chichewa-speaking Africa, is a small-page bible-paper book, with a very strong hard cover. The online version of the Dictionary is being used all over the world. See button above ‘Use Dictionary’. The buttons to the left offer an introduction, information on how to buy the dictionary, and assist on how to learn Chichewa. One button connects you to the history of Chichewa/ Chinyanja dictionary-making (lexicography), with another special button for Johannes Rebmann (1820-1876), a German missionary and church founder in East Africa, who was first to compile a Chichewa/ Chinyanja Dictionary.

Dzina langa ndi Steven Paas (MTh, PhD - Mawu a Mulungu), ine ndine katswiri wa mbiri ya mpingo, komanso wofufuza wa Chichewa/ Chinyanja. M’malo mwa Bungwe la Foundation Heart for Malawi ndikulandirani inu ku webusayiti iyi, imene imapatsa nkhani za Pulojeketi yathu ya Mtanthauziramawu wa Chichewa/ Chinyanja. Msindikizo wachitatu wa dikishonaleyo, yochokera komanso mu Chingerezi (masamba 884, Febuwale 2012), ndi buku la masamba aakulu, la chikuto cholimba, la kolite yapamwamba, limene limagulitsidwa ponseponse. Msindikizo wachinayi (masamba 1152, Ogasiti 2013), makamaka kwa Afirika ya Chichewa/ Chinyanja, ndi buku la masamba aang’ono a mtundi wa mu Baibulo, la chikuto cholimba kwambiri. Dikishonale yolumikizidwa ndi intaneti imagwiritsidwa ntchito ndi anthu ku dziko lonse lapansi. Onani batani yapamwamba. Mabatani a kumanzere amapereka mawu oyamba, nkhani za njira za kugula dikeshonale, komanso chitandizo cha kuphunzira Chichewa. Batani ina imalozera mbiri ya kukonza madikishonale a Chichewa/ Chinyanya (lexicography). Batani yapadera imakulumikizani ndi nkhani za Johannes Rebmann (1820-1876), wamishoni wa Chijeremani amene anakhazikitsa mpingo wa ku Afirika yammawa, komanso anali wokonza wa mtanthauziramawu woyamba wa Chichewa/ Chinyanja.

Dictionary coverMijn naam is Steven Paas (MTh, PhD - Theologie), kerkhistoricus en onderzoeker van het Chichewa-Chinyanja. Namens de stichting Hart voor Malawi verwelkom ik u op deze website, die informatie geeft over ons Chichewa/ Chinyanja woordenboekenproject. De derde editie van het woordenboek, vanuit en in het Engels (884 pagina’s, februari 2012), heeft grote bladzijden, een harde omslag, en is van hoge kwaliteit; het boek is universeel verkrijgbaar. De vierde editie (1152 pagina’s, augustus 2013), speciaal voor Chichewa/ Chinyanja–sprekend Afrika, heeft kleine bladzijden bijbeldrukpapier en een zeer sterke harde omslag. De online versie van het woordenboek wordt geraadpleegd over de hele wereld. Zie de knop rechtsboven. De knoppen links geven informatie over hoe het woordenboek kan worden aangeschaft en hulp over hoe men Chichewa kan leren. Een speciale knop verbindt u met de geschiedenis van het vervaardigen van woordenboeken (lexicografie) in het Chichewa/ Chinyanja. Een speciale knop betreft Johannes Rebmann (1820-1876), Duits zendeling en kerkstichter in Oost-Afrika, die het eerste Chichewa/Chinyanja-woordenboek samenstelde.

 

Project Partners

Centre for Language Studies Centre for Language Studies
Scotland Malawi Partnership Scotland Malawi Partnership
Johannes Rebmann Stiftung Johannes Rebmann Stiftung
Providing a tool for communication in Chichewa/ Chinyanja speaking Africa   Webmaster -  Copyright © 2016 Steven Paas