Your Very First steps in Chichewa - Asking questions Print

Asking where/ how to go

Chonde, mundithandize (Please help me)
Ndasokera (I have lost the way)
Kodi, Zomba Theological College ili kuti? (Where is ZTC?)
Ndikufuna kupita ku Zomba Theological College (I want to go to ZTC)
Kodi, mukudziwa msewu kukapita ku msika? (Do you know the way to the market?)
Kodi, basi ikuyenda kuti? (Where is the bus going?)

Asking what is the time

Kodi, mukudziwa nthawi? (Do you know the time?)
Kodi, pa nthawi yanji basi ifika? (When does the bus arrive?)

Asking what is the price

Mundinene mtengo (tell me the price)
Kodi, ndalama zingati? (What is the price?)
Kodi, mukukhoza kusintha? (Can you change?)
Tumba lili ndi makeedzjie angati? (How many kg is that bag?)
Ndikufuna kugula ziboliboli (I want to buy woodcraft)
Ndikufuna kugula pwhetekele (I want to buy tomatoes)

Asking about the journey

Kodi, mumachokera kuti? (Where are you from?)
Timachokera ku Holland (We are from Holland)
Kodi, munafika ku Malawi liti? (When did you arrive in Malawi?)
Kodi, mudzachoka ku Malawi liti? (When will you leave Malawi?)

Asking about age

Kodi, munabadwa liti? (When were you born?)
Ndinabadwa m'chaka cha 1948 (I was born in 1948)
Kodi, muli ndi zaka zingati (How old are you - letterlijk: How many =
years do you have?)
Ndili ndi zaka 53 (I am 53)

Asking about work/ profession

Kodi, mumagwira ntchito kuti? (Where do you work?)
Ine ndimagwira ntchito mphunzitsi (I work as a teacher)
Kodi, muli ndi ntchito yanji? (Which work are you doing?)
Ndimaphunzira masamu ku sukulu (I teach mathematics at a school)

 

< Back to the course index

 
Providing a tool for communication in Chichewa/ Chinyanja speaking Africa   Webmaster -  Copyright © 2024 Steven Paas